10 Principles Poster Chichewa Version Nov 2011

Ndondomeko Khumi (10)Zokhuzana ndi Bungwe La Rainforest Alliance Zoyenera Kutsatiridwa 9 7 10 4 HEA CEN LTH TRE 6 ...

0 downloads 124 Views 1MB Size
Ndondomeko Khumi (10)Zokhuzana ndi Bungwe La Rainforest Alliance Zoyenera Kutsatiridwa 9

7

10

4

HEA CEN LTH TRE

6

E OFFIC

1

5 HOUSING

2

1.

Kusamala Madera Okhala Komaso Zachilengedwe

2.

Kusamala Zachilengedwe Ngakhale Zing'onozing'ono

3.

Kusamala Zamoyo Za Mu Nkhalango

4.

Kusamala Madzi

5.

Kusamala Olembedwa Ntchito Komaso Kuonetsetsa Kuti Malo Amene Akugwira Ntchitowo Ali Bwino Kwa Ogwira Ntchito

6.

Kuonetsetsa Kuti Malo Ogwilira Ntchito Sakupereka Chiopyezo Ku Umoyo Wa Ogwira Ntchito Komaso Ali Ndi Chitetezo Chokwanira

3

7.

Kuonetsetsa Kuti Ubale Wathu Wakumudzi Uli Bwino

8.

Kukolora Mbewu Zamitundumitundu

9.

Kuteteza Nthaka

10.

Kusamala Zithu Zoipa / Zotaika Zosiyanasiyana